Projekiti ya Mkangano Waukulu 2.0

Tengani mbali ya kugawa mabuku mamiliyoni mu 2023 ndi 2024 kukonzekera kubwera kwaciwiri kwa Yesu.

Cover-Image_NY
iqL1705928575645

Ellen G. White

M’modzi wa iwo anayambitsa Seventh-day Adventist Church

Ndili ndi cilakolako cacikulu kuwona kuti buku ili lagawidwa kwambiri kuposa mabuku ena… pakuti mubuku ili la Mkangano Waukulu, uthenga wothera wocenjeza dziko upelekedwa momveka bwino kupambana mabuku ena.

24k

Zotsitsidwa

122

Zinenero

pTi1706000110755

Ted N. C. Wilson

Pulezidenti, Seventh-day Adventist Church

Ted N. C. Wilson

Pulezidenti, Seventh-day Adventist Church

M’mene mungatengeleko mbali

Sitepesi

Perekani Projekiti ku komiti ya tchalitchi

Sitepesi

Sankhani Malo Kumene Mudzafikira Anthu

Sitepesi

Dongosolo ya katundu umene mufuna kugula

Sitepesi

Gawani

"Ambuye anandikopa ine kuti ndilembe buku ili kotero kuti <strong>mosazengereza<strong/> likhoza kufalitsidwa <strong>mbali iliyonse<strong/> yadziko, cifukwa macenjezo yomwe yalim’buku ili ndiyoyenera kukonzekera anthu kuyima patsiku la Ambuye."

ebB1706110102934

ELLEN G. WHITE, PAMANJA 24, 1891

Tsitsani Buku La Mkangano Waukulu ndi Zonse Zingakuthandizeni

Mkangano Waukulu

Cifupikitso

Kodi mukuganiza kuti dziko likuyenda bwino kapena likuipira-ipirabe? Ncotsadabwitsa kuti anthu ambiri lero akhulupilira kuti dziko ikuipira-ipirabe. N’kutheka kuti kukayikila kwa dziko lonse kubwela cifukwa cacikhalidwe cakumva mauthenga oyipa, kapena mwina tidziwa mkati mwa ife coonadi cimene ciri cofunikira kwambiri cimene cafotokozedwa mkati mwabuku ili: cinthu cina caonongeka kwambiri ndi dziko lathu lapansi pano ndipo mphamvu tilibenso kucikonza.

Mkangano Waukulu sukuwonesa cabe poyera ciyambi cakuwonongeka kwa mtundu wa anthu, koma uululanso kulimbana kokwiya pansi pa mliri ndi ngozi, ciphuphu, kupha anthu ndi ciwonongekeko. Munchito iyi yodabwitsa muzapeza kuti coipa cili ndi nkhope, cabwino cili ndi cipambano kapena ungwazi, ndipo ucimo uli ndi mathero ake. Ngati inu mufuna kukonzekera kutha kwa dziko lino ndi dziko la ulemelero limene lilinkudza, mufunika kuwerenga buku ili.

Cinenero:

Zotsitsidwa Kwambiri

Cover-Image_PT

Cinenero: Portuguese

Cover-Image_FR

Cinenero: French

Cover-Image_ES

Cinenero: Spanish

Cover-Image_DE

Cinenero: German

Cover-Image_CS

Cinenero: Czech

Cover-Image_HU

Cinenero: Hungarian

Cover-Image_TL

Cinenero: Tagalog

Cover-Image_SW

Cinenero: Swahili

Cover-Image_CEB

Cinenero: Cebuano

Mufuna Kuziwa Zambiri?

  • Privacy Policy
  • Legal Notice
  • Trademark and Logo Usage