Projekiti ya Mkangano Waukulu 2.0
Tengani mbali ya kugawa mabuku mamiliyoni mu 2023 ndi 2024 kukonzekera kubwera kwaciwiri kwa Yesu.
Ellen G. White
M’modzi wa iwo anayambitsa Seventh-day Adventist Church
Ndili ndi cilakolako cacikulu kuwona kuti buku ili lagawidwa kwambiri kuposa mabuku ena… pakuti mubuku ili la Mkangano Waukulu, uthenga wothera wocenjeza dziko upelekedwa momveka bwino kupambana mabuku ena.
Zotsitsidwa
Zinenero
Ted N. C. Wilson
Pulezidenti, Seventh-day Adventist Church
Ted N. C. Wilson
Pulezidenti, Seventh-day Adventist Church
M’mene mungatengeleko mbali
Sitepesi
Perekani Projekiti ku komiti ya tchalitchi
Sitepesi
Sankhani Malo Kumene Mudzafikira Anthu
Sitepesi
Dongosolo ya katundu umene mufuna kugula
Sitepesi
Gawani
"Ambuye anandikopa ine kuti ndilembe buku ili kotero kuti <strong>mosazengereza<strong/> likhoza kufalitsidwa <strong>mbali iliyonse<strong/> yadziko, cifukwa macenjezo yomwe yalim’buku ili ndiyoyenera kukonzekera anthu kuyima patsiku la Ambuye."
ELLEN G. WHITE, PAMANJA 24, 1891
Tsitsani Buku La Mkangano Waukulu ndi Zonse Zingakuthandizeni
Cifupikitso
Kodi mukuganiza kuti dziko likuyenda bwino kapena likuipira-ipirabe? Ncotsadabwitsa kuti anthu ambiri lero akhulupilira kuti dziko ikuipira-ipirabe. N’kutheka kuti kukayikila kwa dziko lonse kubwela cifukwa cacikhalidwe cakumva mauthenga oyipa, kapena mwina tidziwa mkati mwa ife coonadi cimene ciri cofunikira kwambiri cimene cafotokozedwa mkati mwabuku ili: cinthu cina caonongeka kwambiri ndi dziko lathu lapansi pano ndipo mphamvu tilibenso kucikonza.
Mkangano Waukulu sukuwonesa cabe poyera ciyambi cakuwonongeka kwa mtundu wa anthu, koma uululanso kulimbana kokwiya pansi pa mliri ndi ngozi, ciphuphu, kupha anthu ndi ciwonongekeko. Munchito iyi yodabwitsa muzapeza kuti coipa cili ndi nkhope, cabwino cili ndi cipambano kapena ungwazi, ndipo ucimo uli ndi mathero ake. Ngati inu mufuna kukonzekera kutha kwa dziko lino ndi dziko la ulemelero limene lilinkudza, mufunika kuwerenga buku ili.
Cinenero:
Zotsitsidwa Kwambiri